nya-x-nyanja_gen_text_reg/17/22.txt

1 line
309 B
Plaintext

\v 22 Pamene anasiliza kukamba nayo, Mulungu anachokapo pali Abrahamu. \v 23 Abrahamu anatenga Ishmayeli mwan wake mwamuna, na bamene bonse banabadwila mumfumba mwake, na bamene bonse banali munyumba mwa Abrahamu, ana dulidwa khanda yao ya kutsogolo pa tsiku yamene ija, monga mwamane mulungu anakambila naye.