nya-x-nyanja_gen_text_reg/48/03.txt

1 line
292 B
Plaintext

\v 3 Yakobo anti yosefe, " Mulungu wa mphamvu anaonekela kuli ine pamalo ya Luz mu Kanaani. Anani dalisa. \v 4 Ana kamba kuli ine, ' Onani, nizaku panga muntu ochuluka, naku kuchulukisa. Niza panga iwe muli maiko Yambili. Niza pasa malo aya kuli bo badwa mu mbuyo mwako na zintu zo yendelela.