|
\v 50 Ndipo Labani ndi Batuele anayankha kuti, Ichi chintu chachokela kwa Yehova: Sitingakambe kwa iwe choipa kapena chabwino. \v 51 Onani, Rebeka ali pamenso pako, mutenge ndipo uyende, kuti ankhale mukazi wa mwana mwana wa bwana wako , mwamene Yehova akambila." |