nya-x-nyanja_gen_text_reg/24/33.txt

1 line
356 B
Plaintext

\v 33 Banamukonzela vakudya, kuti adye, koma anati, sinizadya nikalibe kukamba vamene nifuna kukamba. "Koma Labani anamuuza kuti, "Kamba." \v 34 Anamuuza kuti, ndine wa nchito wa Abrahamu." \v 35 Yehova anamudalisa bwana wanga kwambili ndiponso niolemela. Anamupasa iye nkosa na ng'ombe, siliva na golide, ba nchito bamuna na bakazi, ndi ngamira naba bulu.