nya-x-nyanja_gen_text_reg/10/08.txt

1 line
316 B
Plaintext

\v 8 Kushi anankala Tate wa Nimilodi wamena anali oyamba kuogojetsa pa chalo. \v 9 Anali opaya nyama wa mpamvu pa mansa ya Yehova. Ndiye chifukwa ukambiwa kuti, " Monga nimolodi opaya nyama wa mpamvu pamanso Yehova." \v 10 Malo oyamba ya ufumu yanali Babiloni, Uliki, Aaaaaaaaaaaaaaaakadi, na Kaine, mudela ya Shina.