1 line
525 B
Plaintext
1 line
525 B
Plaintext
\v 15 Ndipo abale ba Yosefe pamene bana one kuti ba tate babo bafa, bana kamba manja ngati Yosefe akati nkalila naukali ise ndipo nakufuna kytibweza ise zoipa zose tina chita kwa eve? \v 16 Sopano bana lamulila ku pezekapo kwa Yosefe. kukamba kuti, "Ba tate banapasa malamulo bakelebe kufa kukamba, \v 17 Uzeni yosefe izi," napapa ba kukukila abale bako machimmoyabo ndi zolakwa zawo pamene bana chita zoipa kuli iwe." Manje napapata ba kukukile ba tumiki ba Mulungu ba batate bako." Yosefe analila pamene bana kamba na beve. |