1 line
460 B
Plaintext
1 line
460 B
Plaintext
\v 18 Pamene chaka china sila, bana bwela kwa ioe chaka chokokhapo ndipo bakamba kwa iye, " Siti zakubisani bwana kuti ndalama zonse zantu ndipo ngombe zonse ndi za bwana wanga kulibe zasalako mumaso bwana, kuchoselako matupi yatu napamene tikhala. \v 19 Nichifukwa chani tizafela pameso panu, ise pamozi na dziko yatu? Tiguleni, ndipo ise na dziko tizikhala banchito ba Farao. Tipaseni chakudya kuti tinkale namoyo kuti tisafe, na malo asankhala alibe kantu." |