nya-x-nyanja_gen_text_reg/20/06.txt

1 line
359 B
Plaintext

\v 6 Ndipo Mulungu anakamba kuti kwa eve m'maloto, " Ee, niziba naine kuti mu ulemu wa mtima wako wacita ici, ndipo naine ninakulesa kunicimwila. Mwaici sininakuvomeleze iwe kuti umugwire. \v 7 Mwaici, bweza makazi wa munthu, pakuti ni mneneri. Azakupemphelera, ndipo uzankhala moyo. Koma ngati sumubwezela, ziba kuti iwe na ose amene uli nao zoona muzafa."