nya-x-nyanja_gen_text_reg/04/01.txt

1 line
238 B
Plaintext

\c 4 \v 1 Mwamuna anaziba Eva mjukazi wake ndipo anankala na pakati naku bala Kaini. Eva anakamba, "Nabala mwana mwamuna na tandizo ya Yehova." \v 2 Ndipo ana bala mubale wake Abelo. Manji Abelo anankala mu busa koma Kaini ulima mu munda.