1 line
382 B
Plaintext
1 line
382 B
Plaintext
\v 16 Nkhani ya ichi chintu inauzidwa kunyumba kwa Farao: " Ba baleba Yosefe babwela chinakondwelesa Farao na ba nchito bake kwambili. \v 17 Farao anati Yosefe, " Uza ba bale bako chitani ichi: Longani pa nyuma zanu ndipo muyende ku ziko ya Kanani. \v 18 Tengani batate banu na banja ndipo mubwele kwa ine. Nizakupasani vabwino va mu malo la Igupto, ndipo muzadya zonona zamu ziko.' |