1 line
502 B
Plaintext
1 line
502 B
Plaintext
\v 9 Esau anakamba, " Nili nazo zokwanila, mbale wanga. Zisungele zonse zamene ulinazo." \v 10 Yakobo anakamba, " Yai, napapata, Ngati napeza mwayi pa menso panu, nipempa kuti mulandile mpaso iyi yofumila m'manja yanga. 200 nadi naona pa maso pano, cili nga nikuona pa maso pa Mulungu, ndipo mwani landila ine. \v 11 Napapata landilani mpaso yanga yamene nakubweleselani ine, cifukwa Mulungu wacita naine mwa cisomo, ndipo ndili nazo zokwanila," Pamene Yakobo anamupapatila, Esau analandila mpaso ija. |