nya-x-nyanja_gen_text_reg/24/21.txt

1 line
420 B
Plaintext

\v 21 Mwamuna anamulangana iye osakamba kanthu kuona kuti kapena Yehova anamuyendesa bwino mu ulendo wake kapena iai. \v 22 Pamene ngamira zinasiliza kumwa , mwamuna anachosa mpete yapampuno ya golide kulemela kwake sikelo lateka, na vibili va golide vibango vaku manja kwake volemela teni lateka. \v 23 Ndipo anafunsa, "Ndiwe mwana wa bandani? Niuze napapata, kodi kuliko malo kuli ba tate bako kunyumba tigoneko usiku?