nya-x-nyanja_gen_text_reg/24/01.txt

1 line
541 B
Plaintext

\c 24 \v 1 Manje Abrahamu anali anakula maningi ndipo Yehova anamudalisa Abrahamu muvinthu vonse. \v 2 Abrahamu anati kwa wanchito wake, wamene anali mukulu pa nyumba yake ndiponso wamene anali kulamulila zonse anali nazo, "faka kwanja kwako pansi pa chibelo changa. \v 3 Ndipo nizakulapisa iwe pa Yehova, Mulungu wakumwamba, ndi Mulungu wapansi, kuti usakamutengele mukazi mwana wanga mwamuna kuchokela kwa Akenaniwo, mwamene napanga nyumba yanga. \v 4 Koma uzayenda ku Ziko yanga, kuli ba bale banga nakumutengela mukazi mwana wanga Isaki.