|
\v 7 Ndipo Yehova ananena, " Nizacosapo mtundu wa anthu wamene ndina mpanga ine pa calo ca pansi - mtundu wa anthu ndi nyama, ndi zokalaba zonse ndi tunyoni twamwamba, cifukwa nimvela kuipa kuti ninampanga izi." \v 8 Koma Nowah anapeza mwayi pamaso pa Yehova. |