nya-x-nyanja_gen_text_reg/50/18.txt

1 line
434 B
Plaintext

\v 18 Ba bale bake futi ana yenda ndi kugona choyangana pasi pamaso pake. Bana kamba, "One, ndise ba nchito bako." \v 19 Koma Yosefe ana bayanka beve, "Musayope. kodi nilimumalo ya Mulungu? \v 20 Kwa iwe, munanifunila zoipa ine. Koma ana ni funila zabwino. Ku pulumusa miyo zaanthu ambili. Monga muona lelo. \v 21 Manje musayope nizakupasane vintu iwe na bana bangona anabalikisa beve munila yambwinno akukamba zabwino ku mitima yabo.