nya-x-nyanja_gen_text_reg/41/07.txt

1 line
339 B
Plaintext

\v 7 Mitu yofota inamela ngala zisanu ndi ziwili zija zabwino koma futi zozula. Pamene Farao anauka, onani, yanali chabe maloto. \v 8 Ndipo kuseniseni muzimu wake unavutika maningi. Anatumiza kukaitana bamasenga pamozi na banzelu bonse ba ku Aigupto. Farao anabawuza beve maloto yake, koma panalibe wamene anakwanisa kumumangusulila Falao.