\c 38 \v 1 Inabwela ntawi pomwe Yuda anasiya abale bake nonkhala kuli omwe anali na zina la Hira. \v 2 Anapeza kuja mwana mukazi wa mwamuna waku Kenaani anali na zina la Shuwa. Anamutenga ndipo anamungela.