nya-x-nyanja_gen_text_reg/02/15.txt

1 line
309 B
Plaintext

\v 15 Yehova Mulungu anatenga mwamuna naku muika mu munda wa Eden kuti azisebenzamo naku sungamo. \v 16 Yehova Mulungu mwamuna, kuti, "ndiwe omasuka kudya kuli mutengo uli onse wa munda. \v 17 Koma kuchokela mu mutengo oziba vabwino na voipa osadya chifukwa siku yamene uzakadyaako, zoona zoona uzaka mwalila.