1 line
333 B
Plaintext
1 line
333 B
Plaintext
\v 34 Siku yokonkapo woyambila anawuka mung'ono, "nvela, nonangona nabatate usiku wapita, Tiye tibamwese moba lelo usiku nafuti, ndipo uzayenda kugona nabo, kuti tisunge mbwe yabatate batu." \v 35 Uja usiku nawo banapasa batate bawo moba, ndipo mung'ono anayenda kugona nabatate bawo. Batate bake sibanazibe pe anagona na pe anawuka. |