|
\v 12 Bamuna banakamba kuli Loti. "uliko nawuliwonse pano? Mupongozi mwamuna, mwna mwamuna, mukazi na uliwonse wako mumuzinda, bachose pano. \v 13 Tifuna kuwononga malo ano, chifukwa kulila kwawo kwavenka mamingi kuli yehova ndipo atituma kuti tiwononge malo ano." |