nya-x-nyanja_gen_text_reg/03/04.txt

1 line
430 B
Plaintext

\v 4 Njoka inakamba ku muzimai," Simuzamwalila. \v 5 Pakuti mulungu aziwa kuti tsiku muzakadya mesnso yako ya zakasenguka, ndiposo uzaka nkhala monga mulungu, kuziba voipa na vabwino. \v 6 " Pamene muzimai anaona kuti mtengo niwabwino kudya, ndipo nio kondweresa menso, ndipo mtengo wenze wopasa cilako lako copusa munthu nzelu, mukazi anatengapo cipaso anadya anadya ndipo anapasako mwamuna wake wamene enze na eve, ndipo anadya.