1 line
391 B
Plaintext
1 line
391 B
Plaintext
\v 14 Cina citika kuti pamene Abramu anagena mu Eygpito, AiEygpito anaona kuti Sarai anali wokongola maningi. \v 15 Pamene bana bamuna ba Farao bana muona, naku mutamanda kuli Farao, naku mupeleka muzimai mu nyumba ya Farao. \v 16 Cifukwa ca eve, Falao anamucitila va bwino Abramu, ndipo Abramu analandila mbelele na ngombe, abulu amuna, anchito amuna, anchito akazi, abulu akazi na ngamila. |