1 line
346 B
Plaintext
1 line
346 B
Plaintext
\c 40 \v 1 Zinabwela pambuyo patapita ivi vintu, wopelekela chakumwa kwa mfumu ya ku Igupto ndi wopanga buledi anakalipisa bwana wawo, mfumu ya ku Igupto. \v 2 Farao anakalipila banchito bake bakulu bakulu babili, mukulu opeleka chakumwa na mukulu bopanga buledi. \v 3 Anabaika mu jele mu nyumba ya malonda mukulu, mu jele mwamene Yosefe analili. |