1 line
361 B
Plaintext
1 line
361 B
Plaintext
\c 31 \v 1 Ndipo Yakobo anamva mau ya bana ba Labani, yamene banakamba, "Yakobo atenga vonse va batate bathu, apeza chuma conse ici kuckela mu vinthu va batate. \v 2 Yacobo anaona kayang'anidwe pa menso pa Laban. Anaona kayang'anidwe kake kanacinja. \v 3 Ndipo anatuma ndi kuitana Rakele ndi bwelala kuziko ya batate bako na ba bale bako ndipo nizankhala naiwe. |