2 lines
309 B
Plaintext
2 lines
309 B
Plaintext
Adamu ana Ziba mukadzi wake nafuti, ndipo mukadzi wake abala mwana wina mwamuna. Anamu pasa zina yakuti Seti nakukamba kuti, "Mulungu anipasa mwana mwamuna winangu pamalo ya Abelo, chifukwa Kaini anamu paya." Mwana mwamuna anabadwa kuli Seti amanupasa dzina yakuti Enosi. Panthawi iyo banthu banayamba kuyi
|
|
|