nya-x-nyanja_gen_text_reg/30/22.txt

1 line
291 B
Plaintext

\v 22 Mulungu anakamba na Recho mumaganizo naku munvelela. \v 23 Anamulengesa kuti ankale na mimba. Anankala na mimba nakunkala na mwana mwamuna. Anakamba kuti "Mulungu anichosa nsoni zanga." \v 24 Anamuitana zina yake Yosefe, kukamba, kuti, "Yawe alundilapo kuli ine mwana mwamuna winangu."