1 line
372 B
Plaintext
1 line
372 B
Plaintext
\v 13 Pasiku yamene iya Nowa bana bake mbamuna, Shemu, Hamu ndi Jafeti namukazi wa Nowa ndi bakazi ba bana ba Nowa banangena mu Chomba. \v 14 Bana ngena pamozi ndi nyama zamu sanga kulingana ndi mutundu wake, ndi zonse zo beta, kulinga na ndi mutundu wake, ndi zokwaba kulinga ndi mutundu wake, ndi nyoni zonse kulingana ndi mutundu wake ndi zina zolengedwa na mapipippo. |