\v 3 Pamene apo Abrahamu anayamuka na ku cokako kwa mukazi wake wokufa, na kunena ku bana ba A'Heti, kuti, \v 4 " Ndine mulendo pakati panu. Nipasenikoni malo ya manda pakati pa imwe, kuti ni ike wanga okufa.