nya-x-nyanja_gen_text_reg/20/15.txt

1 line
318 B
Plaintext

\v 15 Abimeleki anakamba kuti, " Ona, malo bangaali m'manja mwako. Nkhala paliponse pamene pazakukondwelesa." \v 16 Kwa Sara anakamba kuti, " Ona, napasa wobadwa naye wako ma sauzande ya silive. Ici nikuvinikila zolakwa pali iwe mu menso mwa onse bali na iwe, na pamenso pa aliyense, wapangiwa wonkhalilatu wolungama."