nya-x-nyanja_gen_text_reg/20/01.txt

1 line
415 B
Plaintext

\c 20 \v 1 Abrahamu anacokako kuja kupita ku malo ya Nagev, ndipo anankhala pakati padesi na suri. Enze mulendo wonkhala mu Gerari. \v 2 Abrahamu anakamba pali Sara mkazi wake, " Uyu ninabadwa naye." Abimeleki mfumu ya Gerari anaitana Sara na kumtenga. \v 3 Koma Mulungu anabwela kwa Abimeleki mu maloto usiku, na kuti kwa eve, " Ona, ndiwe munthu wokufa cifukwa ca mkazi wamene watenga, pakuti ni mkazi wa munthu."