nya-x-nyanja_gen_text_reg/45/27.txt

1 line
260 B
Plaintext

\v 27 Bana mu uza mau yonse ya Yosefe yamene ana bauza. Pamene yakobo anaona ma kochikali yamene Yosefe anatuma kumutengelapo, muzimu wa Yakobo tate wawo unauka. \v 28 Israeli anati, " Zakwana. Yosefe mwana wanga akali moyo. Nizayenda mukumuona nikalibe kufa.