nya-x-nyanja_gen_text_reg/33/12.txt

1 line
458 B
Plaintext

\v 12 Ndipo Esau anakamba, "Tiyeni tiyambepo kuyenda, ine nizakhala pa songolo panu." \v 13 Yakobo anamu uza iye, " Mbuye wanga zibani ici kuti bana nibang'ono, ndi mbelele ndi ng'ombe zinyonsha tubana. Ngati tizayenda mwa mpavu cukanga siku imodzi cabe zibeto zizafa. \v 14 Napapata lekani bwana ayende patsongolo pa kapolo wanu. Nizayenda pangono pang'ono, ngani mwazibeto zamene zili ku songolo, ndi monga bana, kufikila tifike kwa bwana wanga ku Seiri."