nya-x-nyanja_gen_text_reg/33/06.txt

1 line
343 B
Plaintext

\v 6 Ndipo banchito akazi banafika pamodzi ndi bana bawo ndipo banagwanda pansi. \v 7 Wokonkhapo anali Leya ndi bana bake anafika ndi kukwanda pasi. Posilizila Yosefe na Rakele ana bwela na kugwanda. \v 8 Esau anakamba, " Utanthauza ciani pa banthu wonse aba bambili nakumana nao?" Yakobo anakamba, " Kuti nipeze mwayi pameso pa bwana wanga."