1 line
306 B
Plaintext
1 line
306 B
Plaintext
\v 4 Esau anamutamangila iye, na kumukumatila, na kumulandila ndi kumufyofyonta. Ndipo iwo analila. \v 5 pamene Esau anayangana ku sogolo, anaona azimai ndi bana. Iye anakamba, " Nindani awa banthu amene bali na iwe? " Yakobo anakamba, " Aba ni bana amene Mulungu mwacisomo cake anapasiwa na wancito wanu." |