nya-x-nyanja_gen_text_reg/25/24.txt

1 line
325 B
Plaintext

\v 24 Pamene nthawi yobala inakwana, Taonani, mwenze ba mpundu mu vumo. \v 25 Mwana woyamba anacoka wofiila monse monga chovala camasaku, ndipo ana mupasa zina yake Esau. \v 26 Pambuyo pake mubale wake anacoka, kwanja kwake kunagwira kadenene ka Esau. Anapasiwa zina ya Yakoba. Isaki enze nazaka 60 pamene mkazi wake anabala.