nya-x-nyanja_gen_text_reg/14/13.txt

1 line
392 B
Plaintext

\v 13 Ndipo umozi anapulumuka anam'bweza kuyenda ku udza Abramu mu Hebeli. Wamene anali kunkala pakati pa mitengo yaku mamule, mu Amolite, anali m'bale wa Eshukolo na ana, bonse pamodzi banali kumbali ya Abramu. \v 14 Apo pamene Abramu anavela kuti bodani bagwila mbululu wake, anasongolela amuna bopuzisiwa bo nkondo bobodwila mu banja yake bokwana 318, ndipo anapisha bodani m'paka ku Dani.