nya-x-nyanja_gen_text_reg/17/12.txt

1 line
530 B
Plaintext

\v 12 Bana bonse bamuna bali namatsiku eyiti afunika kudulidwa, mumibado zabantu bako bonse. Kuikilapo na onse obadwa munyumba mwako na iwo amene aguliwa na ndulama kuli alendo amene si obadwa kwa iwe pa mbuyo pako. \v 13 Mwamuna amene abadwa munyumba mwako na wamene waguliwa na ndalama afunika kudulidwa. Mwaicho chipangano changa chizankhala mu nkhanda yanu mu chipangano chosasila. \v 14 Mwamuna aliyense wamene sanadulidwe na mu dulidwe wakanda yakusogolo afunika kuchotsedwa pakati pa bantu bake. Apwanya chipangano chonga."