nya-x-nyanja_gen_text_reg/39/16.txt

1 line
277 B
Plaintext

\v 16 Ana ika chovala chake pafupi na eve mpaka ba bwana bake ba bwela ku nyumba. \v 17 Anamu londolela izi, " Mu Hebeli wa nchito wamene unaleta kuli ise, eze abwela kuni sobelesa. \v 18 Zabwela za chitika kuti pamene napunda, ataba kusiya chovala chake naine, atabila panja."