nya-x-nyanja_gen_text_reg/39/03.txt

1 line
247 B
Plaintext

\v 3 Abwana bake bana ona kuti Yehova anali na Yosefe na zonse zamene anali kuchita yehova ana chulukisa. \v 4 Yosefe anapeza mwai. Anamu sebezela Potifa. Potifa anapanga Yosefe bwana wapa nyumba yake, navonse vintu vake, anavi ika mu manja mwake.