|
\v 3 Rubeni, ndiwe mwana wanga oyamba, mpamvu yanga, na kuyamba kwa mpamvu yanga, ulemu opambana na mpamvu yopambana. \v 4 Osauzika monga manzi oyenda na mpamvu suzapambana, chifukwa unakwela pa bedi ya batate bako. Pamene unaipisa; unakwela pa bedi panga. |