nya-x-nyanja_gen_text_reg/43/11.txt

1 line
378 B
Plaintext

\v 11 Atate babo Israeli ana kamba kwabeve, ngati cinkhala chocho, maje chitani ici. Tangani zabwino mulomuno mumasaka. Pelekani pasi kwa munthu uyu paso zina baimu ndi uchi. Zonukilisa ndi maya, pistachio nati ndi almondi. \v 12 Tengani dalama mupatikizapo mu manja yanu. Dalama ina bwe zalewa pamene muna segula masaka yanu. Zinyamuleni futi mumaja yanu. Kapena ana sokoneza.