nya-x-nyanja_gen_text_reg/43/08.txt

1 line
404 B
Plaintext

\v 8 Yuda anakamba kwa Israeli, tate wake. " Mutumeni mwana na ife, tiza yamuka ndi ku yenda kuti ti nkhale moyo ndi kuti ti safe, bose ife, naimwe, ndi oso bana bathu. \v 9 Niza khala chosimikizilako kwa eve. Muza Muzanipasa muladu ine. Ngati siniza bwaza kwainu kumuonsa pamaso panu, ndipo lekani niyamule dadaulo muyaya. \v 10 Angati sitina chedwe, choonadi ziko tawi asembe ti baleko kuno kaci bili."