1 line
305 B
Plaintext
1 line
305 B
Plaintext
\v 16 Pamene mukulu opanga bulendi anaona kuti kuvumbulusa kunali bwino, anati kwa Yosefe, " Naine nenze na chiloto ndipo, onani mabasiketi yatatu ya buledi yanali pa mutu panga. \v 17 Mu basiketi ya pamwamba munali zosiyana siyana za kudya za Farao, koma tunyomi tunadya mu basiketi inali pa mutu panga." |