\v 12 Yosefe anati kwa iye, iyi ndiye tantauzo lake. Ntambi zitatu ni masiku atatu. \v 13 Mu masiku yatatu Farao azakuchosa mu jele nakukubweza pa chito yako uzaika chiko mumanja mwa Farao, monga mwamene unalili opeleka chakumwa.