nya-x-nyanja_gen_text_reg/31/51.txt

1 line
425 B
Plaintext

\v 51 Labani anakamba kuli Yakobo, " Yangana pamwamba, ndipo ona pa pila, yamene naika pakati kaiwe naine. \v 52 Iyi nthutu ndiye kamboni, na pila ni kamboni kuti sinaza jumpa iyi nthutu kubwera kuli iwe, ndipo na iwe suza jumpa iyi nthutu ku bwela kuli ine, kucita voipa. \v 53 Leka Mulungu wa Abrahamu, na Mulungu wa Nahor, na milungu za ba tate bao, ziweruza pakati kathu." Ndipo Yakobo analapa pakuyopa batate bake Isaki.