nya-x-nyanja_gen_text_reg/31/48.txt

1 line
415 B
Plaintext

\v 48 Labani anakamba, izi miyala ni kamboni pakati kaiwe naine, lelo "Cifukwa cake zina yake baitanapo Giliyadi. \v 49 Paitaniwanso mizipa cifukwa Labani anakamba, Leka Yehova ayangane pakati kaiwe na ine, pamene tisiyana wina na muzake. \v 50 Ngati suzasunga bana banga bakazi bwino, olo uzatenga bakazi bena pambali ya bana banga bakazi, loko palibe wina ali naise, ona, Mulungu ni kamboni pakati kaiwe na ine."