|
\v 54 Ndipo iye na bamuna anali nawo ba nadya na kumwa. Banankhala kuja usiku bonse, ndipo pamene banauka kuseni, anati, nitumeni kwa bwana wanga. \v 55 Mubale wake na ba Mai bake banati, lekani mukazi mun'gono ankhale naife masiku yang'ono masiku yali teni. |