|
\v 26 Mwamuna anagwada na kuyamika Yehova. \v 27 Anati, adalisike Yehova Mulungu wa bwana wanga Abrahamu, wamene sanakane ku kulupilika kwa chipangano ndi chifundo chake mwa bwana wanga. Koma monga ine , Yehova anisogolela munjila ya kunyumba ya ba bale ba bwana wanga. |