|
\v 9 Mu ngelo wa Yehova ana kamba nae. " Bwelela kuli okulemba chito wako. Zipeleke na kuzi chepesa ku ulomulilo wake." \v 10 Ndipo mu ngelo wa Yehova ana kamba nae, " ni zaku chulukisa kwabili obabadwa kwaiwe. Kuti ba ka khale bubili ochuka osabelengeka." |