nya-x-nyanja_gen_text_reg/09/16.txt

1 line
301 B
Plaintext

\v 16 Utawalenza uzakala mumakumbi koma ndipo niza wo ona kuti nikumbukile chipangano chamuyaya chilipakati pamulungu nachose chamoyo chilegedwe chili paziko yapansi." \v 17 Ndipo mulungu kuli Nowa, "Ichi diye chozibisa chipangano chamene ninavomekeza pali ine na vonse vilegedwe va pazinko yapansi."